Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Anachitanso chimodzimodzi ndi kapu+ atadya chakudya chamadzulo, ndipo anati: “Kapu iyi ikutanthauza pangano latsopano+ pamaziko a magazi anga.+ Muzichita zimenezi nthawi zonse pamene mukumwa za m’kapu imeneyi pondikumbukira.”+

  • Agalatiya 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+

  • Aefeso 5:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Anatero kuti iyeyo alandire mpingowo uli wokongola ndiponso waulemerero,+ wopanda banga kapena makwinya kapenanso chilichonse cha zinthu zotero, koma kuti ukhale woyera ndi wopanda chilema.+

  • Aheberi 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti iye sakuthandiza angelo ngakhale pang’ono, koma akuthandiza mbewu ya Abulahamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena