2 Akorinto 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuti Satana asatichenjerere,+ pakuti tikudziwa bwino ziwembu zake.+ 1 Timoteyo 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso, akhale woti ngakhale anthu akunja* akumuchitira umboni wabwino,+ kuti asatonzedwe ndi kukodwa mumsampha+ wa Mdyerekezi.
7 Komanso, akhale woti ngakhale anthu akunja* akumuchitira umboni wabwino,+ kuti asatonzedwe ndi kukodwa mumsampha+ wa Mdyerekezi.