Agalatiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+ 1 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.
7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+
14 Usamanyalanyaze mphatso+ imene uli nayo, yomwe unapatsidwa mwaulosi+ ndiponso pamene bungwe la akulu linaika manja+ pa iwe.