Machitidwe 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho Paulo anakhalabe m’nyumba yake yolipira kwa zaka ziwiri zathunthu,+ ndipo onse obwera kudzamuona anali kuwalandira ndi manja awiri.
30 Choncho Paulo anakhalabe m’nyumba yake yolipira kwa zaka ziwiri zathunthu,+ ndipo onse obwera kudzamuona anali kuwalandira ndi manja awiri.