Akolose 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+ 1 Yohane 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera,+ ndipo anatipatsa nzeru+ kuti timudziwe woonayo.+ Ndipo ife ndife ogwirizana+ ndi woonayo, kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu. Iyeyo ndiye Mulungu woona+ ndiponso wopereka moyo wosatha.+
9 N’chifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinaleke kukupemphererani.+ Takhala tikupemphanso kuti mukhale odziwa molondola+ chifuniro chake, ndiponso kuti mukhale ndi nzeru+ zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+
20 Tikudziwa kuti Mwana wa Mulungu anabwera,+ ndipo anatipatsa nzeru+ kuti timudziwe woonayo.+ Ndipo ife ndife ogwirizana+ ndi woonayo, kudzera mwa Mwana wake Yesu Khristu. Iyeyo ndiye Mulungu woona+ ndiponso wopereka moyo wosatha.+