Yesaya 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Mpando wachifumu ndithu udzakhazikika ndi kukoma mtima kosatha.+ Mfumu idzakhala pampandowo n’kumalamulira mokhulupirika muhema wa Davide.+ Izidzaweruza n’kumafunafuna chilungamo, ndipo izidzachita mwachangu zinthu zoyenera.”+ Aheberi 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anali wokhulupirika+ kwa Mulungu amene anamuika kukhala mtumwi ndi mkulu wa ansembe, monga mmenenso Mose+ analili wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu.+
5 “Mpando wachifumu ndithu udzakhazikika ndi kukoma mtima kosatha.+ Mfumu idzakhala pampandowo n’kumalamulira mokhulupirika muhema wa Davide.+ Izidzaweruza n’kumafunafuna chilungamo, ndipo izidzachita mwachangu zinthu zoyenera.”+
2 Iye anali wokhulupirika+ kwa Mulungu amene anamuika kukhala mtumwi ndi mkulu wa ansembe, monga mmenenso Mose+ analili wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu.+