Salimo 72:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aweruzire anthu milandu mwachilungamo,+Ndipo aweruze milandu ya osautsika ndi ziweruzo zolungama.+ Yesaya 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Taonani! Mfumu+ idzalamulira mwachilungamo,+ ndipo akalonga+ adzalamuliranso mwachilungamo.