Ekisodo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mukapange chihema chopatulika ndi ziwiya zake mogwirizana ndendende ndi zonse zimene ndikukusonyeza.+ Salimo 84:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Inu Yehova wa makamu,+Ine ndimakondadi chihema chanu chachikulu!+ Aheberi 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 N’zoona kuti nyumba iliyonse inamangidwa ndi winawake, koma amene anapanga zinthu zonse ndi Mulungu.+
9 Mukapange chihema chopatulika ndi ziwiya zake mogwirizana ndendende ndi zonse zimene ndikukusonyeza.+
4 N’zoona kuti nyumba iliyonse inamangidwa ndi winawake, koma amene anapanga zinthu zonse ndi Mulungu.+