Genesis 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7. Analipatula kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli, iye wakhala akupuma pa ntchito yake yonse yolenga ndi yopanga zimene anafuna.+ Aefeso 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ndiponso kuti ndionetse anthu mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera.+ Kuyambira kalekale, chinsinsi chimenechi chakhala chobisika mwa —Mulungu, amene analenga zinthu zonse.+
3 Kenako Mulungu anadalitsa tsiku la 7. Analipatula kuti likhale lopatulika, chifukwa kuyambira pa tsikuli, iye wakhala akupuma pa ntchito yake yonse yolenga ndi yopanga zimene anafuna.+
9 ndiponso kuti ndionetse anthu mmene chinsinsi chopatulikacho+ chikuyendetsedwera.+ Kuyambira kalekale, chinsinsi chimenechi chakhala chobisika mwa —Mulungu, amene analenga zinthu zonse.+