Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Yohane 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+
8 Ndimakondwera ndi kuchita chifuniro chanu, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+
38 Chifukwa ndinatsika kuchokera kumwamba+ kudzachita chifuniro cha iye amene anandituma, osati chifuniro changa.+