Yesaya 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu inu limbitsani manja ofooka ndiponso mawondo agwedegwede.+ Aroma 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 kapena kuti tidzalimbikitsane+ mwa chikhulupiriro, chanu ndi changa.+