Aroma 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chitani zimenezi, makamakanso chifukwa chakuti nyengo ino mukuidziwa, kuti tili kale mu ola lakuti mudzuke ku tulo,+ pakuti chipulumutso chathu chili pafupi kwambiri tsopano kusiyana ndi nthawi imene tinakhala okhulupirira.+ 2 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Muzichita zimenezi poyembekezera+ ndi kukumbukira nthawi zonse kukhalapo kwa tsiku la Yehova,+ pamene kumwamba kudzapsa ndi moto n’kusungunuka,+ ndipo zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri n’kusungunuka.
11 Chitani zimenezi, makamakanso chifukwa chakuti nyengo ino mukuidziwa, kuti tili kale mu ola lakuti mudzuke ku tulo,+ pakuti chipulumutso chathu chili pafupi kwambiri tsopano kusiyana ndi nthawi imene tinakhala okhulupirira.+
12 Muzichita zimenezi poyembekezera+ ndi kukumbukira nthawi zonse kukhalapo kwa tsiku la Yehova,+ pamene kumwamba kudzapsa ndi moto n’kusungunuka,+ ndipo zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri n’kusungunuka.