Genesis 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Abele nayenso anabweretsa ana oyamba+ a nkhosa zake n’kuwapereka nsembe, ndipo anaperekanso nsembe mafuta a nkhosazo.+ Yehova anakondwera ndi Abele ndipo analandira nsembe yake,+
4 Abele nayenso anabweretsa ana oyamba+ a nkhosa zake n’kuwapereka nsembe, ndipo anaperekanso nsembe mafuta a nkhosazo.+ Yehova anakondwera ndi Abele ndipo analandira nsembe yake,+