Machitidwe 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yakobo m’bale wake wa Yohane+ anamupha ndi lupanga.+ Aheberi 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komabe, pitirizani kukumbukira masiku akale. Mutalandira kuwala kochokera kwa Mulungu m’masiku amenewo,+ munapirira mayesero aakulu ndi masautso.+
32 Komabe, pitirizani kukumbukira masiku akale. Mutalandira kuwala kochokera kwa Mulungu m’masiku amenewo,+ munapirira mayesero aakulu ndi masautso.+