Levitiko 23:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Muzikhala m’misasa masiku 7.+ Mbadwa zonse za Isiraeli zizikhala m’misasa,+ 1 Petulo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+
11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+