Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Atesalonika 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Timatero pakuti timakumbukira nthawi zonse ntchito zanu zachikhulupiriro,+ ndi ntchito zanu zachikondi. Timateronso pokumbukira mmene munapiririra chifukwa cha chiyembekezo+ chanu mwa Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu wathu ndi Atate.

  • Tito 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mawu amenewa ndi oona,+ ndipo ndikufuna kuti nthawi zonse uzinena zinthu zimenezi motsindika, kuti amene akukhulupirira Mulungu nthawi zonse aziganiza za mmene angapitirizire kuchita ntchito zabwino.+ Zinthu izi n’zabwino ndi zothandiza kwa anthu.

  • Yakobo 1:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma woyang’anitsitsa m’lamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu, amene amalimbikira kutero, adzakhala wosangalala+ polichita chifukwa chakuti sali wongomva n’kuiwala, koma wochita.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena