Akolose 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nthawi zonse mawu anu azikhala achisomo,+ okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire+ wina aliyense.
6 Nthawi zonse mawu anu azikhala achisomo,+ okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire+ wina aliyense.