Mateyu 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Inu ndinu mchere+ wa dziko lapansi. Koma ngati mchere watha mphamvu, kodi mphamvu yake angaibwezeretse motani? Sungagwire ntchito iliyonse koma ungafunike kuutaya kunja+ kumene anthu akaupondaponda. Maliko 9:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mchere ndi wabwino, koma mcherewo ukatha mphamvu, kodi mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere+ mwa inu nokha, ndipo sungani mtendere+ pakati panu.”
13 “Inu ndinu mchere+ wa dziko lapansi. Koma ngati mchere watha mphamvu, kodi mphamvu yake angaibwezeretse motani? Sungagwire ntchito iliyonse koma ungafunike kuutaya kunja+ kumene anthu akaupondaponda.
50 Mchere ndi wabwino, koma mcherewo ukatha mphamvu, kodi mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere+ mwa inu nokha, ndipo sungani mtendere+ pakati panu.”