Aefeso 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi, Yakobo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho gonjerani+ Mulungu, koma tsutsani Mdyerekezi+ ndipo adzakuthawani.+
11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi,