1 Yohane 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene amanena kuti ali m’kuunika koma amadana+ ndi m’bale wake, ndiye kuti ali mu mdima mpaka pano.+ Chivumbulutso 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwe ukunena kuti: “Ndine wolemera,+ ndapeza chuma chambiri ndipo sindikusowa kanthu,” koma sukudziwa kuti ndiwe wovutika, womvetsa chisoni, wosauka, wakhungu,+ ndi wamaliseche.
9 Amene amanena kuti ali m’kuunika koma amadana+ ndi m’bale wake, ndiye kuti ali mu mdima mpaka pano.+
17 Iwe ukunena kuti: “Ndine wolemera,+ ndapeza chuma chambiri ndipo sindikusowa kanthu,” koma sukudziwa kuti ndiwe wovutika, womvetsa chisoni, wosauka, wakhungu,+ ndi wamaliseche.