Miyambo 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zilango anazikhazikitsira anthu onyoza,+ ndipo zikwapu anazisungira msana wa anthu opusa.+ Yuda 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+
10 Koma anthu amenewa amalankhula monyoza zinthu zonse zimene sakuzidziwa bwinobwino,+ ndipo ali ngati nyama zopanda nzeru. Pochita zinthu zawo zonse zimene amazichita mwachibadwa, amakhala ngati nyama+ ndipo mwa kutero amapitiriza kudziipitsa.+