1 Petulo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+ 1 Yohane 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, tiyeni tipitirize kukondana,+ chifukwa chikondi+ chimachokera kwa Mulungu,+ ndipo aliyense amene ali ndi chikondi, ndi mwana wa Mulungu ndipo akudziwa Mulungu.+
23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+
7 Okondedwa, tiyeni tipitirize kukondana,+ chifukwa chikondi+ chimachokera kwa Mulungu,+ ndipo aliyense amene ali ndi chikondi, ndi mwana wa Mulungu ndipo akudziwa Mulungu.+