Yohane 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndithudi ndikukuuza, Zimene ife timadziwa timazilankhula, ndipo zimene taona timazichitira umboni.+ Koma anthu inu simulandira umboni umene timapereka.+
11 Ndithudi ndikukuuza, Zimene ife timadziwa timazilankhula, ndipo zimene taona timazichitira umboni.+ Koma anthu inu simulandira umboni umene timapereka.+