Aefeso 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koposa zonse, nyamulani chishango chachikulu chachikhulupiriro,+ chimene mudzathe kuzimitsira mivi yonse yoyaka moto+ ya woipayo. 1 Yohane 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Lamulo lake ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro m’dzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.
16 Koposa zonse, nyamulani chishango chachikulu chachikhulupiriro,+ chimene mudzathe kuzimitsira mivi yonse yoyaka moto+ ya woipayo.
23 Lamulo lake ndi lakuti, tikhale ndi chikhulupiriro m’dzina la Mwana wake Yesu Khristu+ ndiponso tizikondana,+ monga mmene iye anatilamulira.