Aroma 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+ 1 Atesalonika 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti inu nonse ndinu ana a kuwala+ ndiponso ana a usana.+ Si ife a usiku kapena a mdima ayi.+
12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+