Agalatiya 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Panopa ndikanakonda kukhala pakati panu+ kuti ndilankhule mosiyanako, chifukwa mwandithetsa nzeru.+
20 Panopa ndikanakonda kukhala pakati panu+ kuti ndilankhule mosiyanako, chifukwa mwandithetsa nzeru.+