2 Yohane 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale kuti ndili ndi zambiri zoti ndikulembereni, sindikufuna kuzilemba papepala ndi inki,+ koma ndikuyembekezera kubwera kwa inu kuti ndidzalankhule nanu pamasom’pamaso,+ kuti mudzakhale ndi chimwemwe+ chokwanira.+
12 Ngakhale kuti ndili ndi zambiri zoti ndikulembereni, sindikufuna kuzilemba papepala ndi inki,+ koma ndikuyembekezera kubwera kwa inu kuti ndidzalankhule nanu pamasom’pamaso,+ kuti mudzakhale ndi chimwemwe+ chokwanira.+