3 Yohane 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma ndikuyembekezera kukuona posachedwapa ndipo tidzalankhulana pamasom’pamaso.+ Mtendere ukhale nawe.+ Anzathu kuno akukupatsa moni.+ Iwenso undiperekere moni+ kwa anzathu kumeneko aliyense payekhapayekha.
14 Koma ndikuyembekezera kukuona posachedwapa ndipo tidzalankhulana pamasom’pamaso.+ Mtendere ukhale nawe.+ Anzathu kuno akukupatsa moni.+ Iwenso undiperekere moni+ kwa anzathu kumeneko aliyense payekhapayekha.