Tito 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onse amene ali nane akupereka moni.+ Undiperekere moni kwa anthu amene amatikonda chifukwa cha chikhulupiriro. Kukoma mtima kwakukulu kukhale ndi inu nonse.+
15 Onse amene ali nane akupereka moni.+ Undiperekere moni kwa anthu amene amatikonda chifukwa cha chikhulupiriro. Kukoma mtima kwakukulu kukhale ndi inu nonse.+