Ekisodo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.” Yohane 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inu mumalambira chimene simuchidziwa.+ Ife timalambira chimene tikuchidziwa, chifukwa chipulumutso chikuchokera kwa Ayuda.+ Tito 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikulembera Tito, mwana wanga+ weniweni m’chikhulupiriro chimodzi chomwe tili nacho: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wa Mulungu Atate+ ndi Khristu Yesu Mpulumutsi wathu,+ zikhale nawe. Aheberi 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 tidzapulumuka bwanji+ ngati tanyalanyaza+ chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutso chimenechi,+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.+ 1 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+ 2 Petulo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Simoni Petulo, kapolo+ ndi mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera anthu amene apeza chikhulupiriro chofanana ndi chathu,+ mwa chilungamo+ cha Mulungu wathu ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu.+
6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.”
22 Inu mumalambira chimene simuchidziwa.+ Ife timalambira chimene tikuchidziwa, chifukwa chipulumutso chikuchokera kwa Ayuda.+
4 Ndikulembera Tito, mwana wanga+ weniweni m’chikhulupiriro chimodzi chomwe tili nacho: Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere wa Mulungu Atate+ ndi Khristu Yesu Mpulumutsi wathu,+ zikhale nawe.
3 tidzapulumuka bwanji+ ngati tanyalanyaza+ chipulumutso chachikulu chonchi?+ Ambuye wathu ndi amene anayamba kunena za chipulumutso chimenechi,+ ndipo anthu amene anamumva anatitsimikizira zimenezo.+
9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+
1 Ine Simoni Petulo, kapolo+ ndi mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndikulembera anthu amene apeza chikhulupiriro chofanana ndi chathu,+ mwa chilungamo+ cha Mulungu wathu ndi Mpulumutsi wathu Yesu Khristu.+