Yohane 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe nthawi idzafika, ndipo ndi yomwe ino, pamene olambira oona adzalambira Atate motsogoleredwa ndi mzimu+ ndi choonadi,+ pakuti Atate amafuna oterowo azimulambira.+
23 Komabe nthawi idzafika, ndipo ndi yomwe ino, pamene olambira oona adzalambira Atate motsogoleredwa ndi mzimu+ ndi choonadi,+ pakuti Atate amafuna oterowo azimulambira.+