Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mthandizi ameneyo ndi mzimu wa choonadi.+ Mzimu umenewo dziko silingaulandire,+ chifukwa siliuona kapena kuudziwa. Inu mumaudziwa chifukwa umakhala mwa inu, ndipo uli mwa inu.+

  • Aroma 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mulungu anachita izi kuti ife amene tikuyenda motsatira za mzimu,+ osati motsatira zofuna za thupi, tikwaniritse miyezo yolungama ya Chilamulo.+

  • 2 Akorinto 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 pamene tikuika maso athu pa zinthu zosaoneka, osati pa zooneka.+ Pakuti zooneka n’zakanthawi,+ koma zosaoneka n’zamuyaya.+

  • 2 Akorinto 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 pakuti tikuyenda mwa chikhulupiriro, osati mwa zooneka ndi maso.+

  • Afilipi 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti ife ndife amdulidwe weniweni,+ amene tikuchita utumiki wopatulika mwa mzimu wa Mulungu.+ Timadzitamandira mwa Khristu Yesu,+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena