Maliko 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma inu khalani wochenjera. Anthu adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani m’masunagoge+ ndi kukuimikani pamaso pa abwanamkubwa ndi mafumu chifukwa cha ine, kuti ukhale umboni kwa iwo.+ Chivumbulutso 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Umaonetsanso kupirira,+ ndipo walimbana ndi mavuto osiyanasiyana chifukwa cha dzina langa,+ koma sunafooke.+
9 “Koma inu khalani wochenjera. Anthu adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani m’masunagoge+ ndi kukuimikani pamaso pa abwanamkubwa ndi mafumu chifukwa cha ine, kuti ukhale umboni kwa iwo.+
3 Umaonetsanso kupirira,+ ndipo walimbana ndi mavuto osiyanasiyana chifukwa cha dzina langa,+ koma sunafooke.+