Mateyu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+ Luka 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Koma zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani ndi kukuzunzani,+ adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakutengerani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+ 2 Timoteyo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+
9 “Kenako anthu adzakuperekani ku chisautso+ ndipo adzakuphani.+ Mitundu yonse idzadana nanu+ chifukwa cha dzina langa.+
12 “Koma zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani ndi kukuzunzani,+ adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakutengerani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+
12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mwa Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+