Luka 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Chotero ndikukuuzani kuti, Aliyense wovomereza+ pamaso pa anthu kuti ali kumbali yanga, Mwana wa munthunso adzavomereza pamaso pa angelo a Mulungu kuti ali kumbali yake.+ Yohane 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Mitima yanu isavutike.+ Khulupirirani Mulungu,+ khulupiriraninso ine.+ 1 Yohane 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Amene wavomereza+ Mwana amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+
8 “Chotero ndikukuuzani kuti, Aliyense wovomereza+ pamaso pa anthu kuti ali kumbali yanga, Mwana wa munthunso adzavomereza pamaso pa angelo a Mulungu kuti ali kumbali yake.+
23 Aliyense amene amakana Mwana sangakhale pa ubwenzi ndi Atate.+ Amene wavomereza+ Mwana amakhalanso pa ubwenzi ndi Atate.+