Chivumbulutso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Efeso,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena wonyamula nyenyezi 7+ m’dzanja lake lamanja, woyenda pakati pa zoikapo nyale 7 zagolide.+
2 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Efeso,+ lemba kuti: Izi ndi zimene akunena wonyamula nyenyezi 7+ m’dzanja lake lamanja, woyenda pakati pa zoikapo nyale 7 zagolide.+