Machitidwe 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera a kumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena, Aefeso 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu mwa chifuniro cha Mulungu,+ ndikulembera oyera amene ali ku Efeso, okhulupirikawo+ okhala mogwirizana+ ndi Khristu Yesu, kuti:
19 Nthawi inayake, Apolo+ ali ku Korinto, Paulo anadzera kumadera a kumtunda mpaka anafika ku Efeso.+ Kumeneko anapezako ophunzira ena,
1 Ine Paulo, mtumwi+ wa Khristu Yesu mwa chifuniro cha Mulungu,+ ndikulembera oyera amene ali ku Efeso, okhulupirikawo+ okhala mogwirizana+ ndi Khristu Yesu, kuti: