Yohane 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+ Yohane 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndine mtengo wa mpesa, inu ndinu nthambi zake. Amene ali wolumikizika kwa ine, inenso n’kukhala wolumikizika kwa iye, ameneyo amabala zipatso zochuluka,+ chifukwa simungathe kuchita kalikonse popanda ine.
4 Khalani ogwirizana ndi ine, inenso ndikhala wogwirizana ndi inu.+ Nthambi singabale zipatso payokha, pokhapokha ngati ndi yolumikizikabe kumpesawo. Chimodzimodzi inunso, simungabale zipatso mukapanda kukhala olumikizika kwa ine.+
5 Ine ndine mtengo wa mpesa, inu ndinu nthambi zake. Amene ali wolumikizika kwa ine, inenso n’kukhala wolumikizika kwa iye, ameneyo amabala zipatso zochuluka,+ chifukwa simungathe kuchita kalikonse popanda ine.