Yohane 6:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Munthu wakudya mnofu wanga ndi kumwa magazi anga, iyeyo ndi ine timakhala ogwirizana.+ 1 Akorinto 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano inu ndinu thupi la Khristu, ndipo aliyense wa inu ndi chiwalo cha thupilo.+ Akolose 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amatero koma osagwira mwamphamvu amene ali mutu,+ amene kuchokera kwa iye, thupi lonselo, limene limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ndi lolumikizika bwino+ mwa mfundo zake ndi minyewa, limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+
19 Amatero koma osagwira mwamphamvu amene ali mutu,+ amene kuchokera kwa iye, thupi lonselo, limene limapeza zonse zimene limafunikira ndipo ndi lolumikizika bwino+ mwa mfundo zake ndi minyewa, limakulabe mothandizidwa ndi Mulungu.+