Aroma 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+ Aefeso 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 umene ndi thupi lake.+ Mpingowo ndi wodzaza+ ndi iye, amene amadzaza zinthu zonse mokwanira.+ Akolose 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+
5 momwemonso ifeyo, ngakhale kuti ndife ambiri, tili thupi limodzi+ mwa Khristu, ndipo aliyense payekha ndi chiwalo cha mnzake.+
24 Ndikusangalala tsopano ndi masautso amene ndikukumana nawo chifukwa cha inu.+ Ndipo inenso kumbali yanga, ndikuona kuti sindinazunzikebe mokwanira+ monga chiwalo cha thupi la Khristu, limene ndi mpingo.+