Chivumbulutso 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo akulu 24 aja,+ amene anali atakhala pamipando yawo yachifumu pamaso pa Mulungu, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo analambira Mulungu+
16 Ndipo akulu 24 aja,+ amene anali atakhala pamipando yawo yachifumu pamaso pa Mulungu, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo analambira Mulungu+