Yesaya 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Wagwa kuchokera kumwamba,+ wonyezimirawe, iwe mwana wa m’bandakucha! Wadulidwa n’kugwera padziko lapansi,+ iwe amene unali kupundula mitundu.+ Luka 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno iye anawauza kuti: “Ndinayamba kuona Satana atagwa+ kale ngati mphezi kuchokera kumwamba. 2 Akorinto 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo zimenezo n’zosadabwitsa, popeza ngakhale Satana amadzisandutsa mngelo wa kuwala.+
12 “Wagwa kuchokera kumwamba,+ wonyezimirawe, iwe mwana wa m’bandakucha! Wadulidwa n’kugwera padziko lapansi,+ iwe amene unali kupundula mitundu.+