-
Zekariya 4:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndinamufunsanso kuti: “Kodi nthambi ziwiri izi za mitengo ya maolivi, zimene zikuthira mafuta agolide m’mbale yolowa kudzera m’mapaipi awiri agolide, zikuimira chiyani?”
-