Chivumbulutso 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chinaloledwa+ kuchita nkhondo ndi oyerawo ndi kuwagonjetsa.+ Chinapatsidwanso ulamuliro pa anthu a fuko lililonse, mtundu uliwonse, chinenero chilichonse ndi dziko lililonse. Chivumbulutso 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+
7 Chinaloledwa+ kuchita nkhondo ndi oyerawo ndi kuwagonjetsa.+ Chinapatsidwanso ulamuliro pa anthu a fuko lililonse, mtundu uliwonse, chinenero chilichonse ndi dziko lililonse.
15 Kenako mngeloyo anandiuza kuti: “Madzi amene wawaona aja, pamene hule lija lakhala, akuimira mitundu ya anthu, makamu, mayiko, ndi zinenero.+