Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako anandiuza kuti: “Ine ndikudziwitsa zimene zidzachitike kumapeto kwa nthawi yopereka chiweruzo, chifukwa chakuti masomphenyawo adzakwaniritsidwa pa nthawi yoikidwiratu ya mapeto.+

  • Mika 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 M’masiku otsiriza,+ phiri+ la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri, ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu ya anthu idzakhamukira kumeneko.+

  • Mateyu 24:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndithu ndikukuuzani kuti m’badwo uwu+ sudzatha wonse kuchoka kufikira zinthu zonsezi zitachitika.

  • Aroma 16:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mulungu amene amapatsa mtendere+ aphwanya Satana+ pansi pa mapazi anu posachedwapa. Kukoma mtima kwakukulu kwa Ambuye wathu Yesu kukhale ndi inu.+

  • 2 Timoteyo 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma dziwa kuti, masiku otsiriza+ adzakhala nthawi yapadera komanso yovuta.+

  • 2 Petulo 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choyamba, inu mukudziwa kuti m’masiku otsiriza+ kudzakhala onyodola+ amene azidzatsatira zilakolako zawo,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena