Tito 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera+ ndi kumvera maboma ndiponso olamulira.+ Komanso akhale okonzekera ntchito iliyonse yabwino.+ Chivumbulutso 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+
3 Pitiriza kuwakumbutsa kuti azigonjera+ ndi kumvera maboma ndiponso olamulira.+ Komanso akhale okonzekera ntchito iliyonse yabwino.+
11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+