Luka 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo aliyense wonena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma wonyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa.+
10 Ndipo aliyense wonena mawu onyoza Mwana wa munthu, adzakhululukidwa. Koma wonyoza mzimu woyera sadzakhululukidwa.+