Machitidwe 7:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 “Makolo athuwo anali ndi chihema cha umboni m’chipululu. Anachipanga potsatira malangizo amene Mulungu anapereka pamene anali kulankhula ndi Mose. Mulungu anauza Mose kuti apange chihemacho molingana ndi chithunzi chimene anachiona.+
44 “Makolo athuwo anali ndi chihema cha umboni m’chipululu. Anachipanga potsatira malangizo amene Mulungu anapereka pamene anali kulankhula ndi Mose. Mulungu anauza Mose kuti apange chihemacho molingana ndi chithunzi chimene anachiona.+