Chivumbulutso 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo onse okhala padziko lapansi adzachilambira. Anthu onsewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu+ wa moyo, umene Mwanawankhosa amene anaphedwa,+ ndiye mwiniwake. Mpukutuwo unakonzedwa kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+
8 Ndipo onse okhala padziko lapansi adzachilambira. Anthu onsewa mayina awo sanalembedwe mumpukutu+ wa moyo, umene Mwanawankhosa amene anaphedwa,+ ndiye mwiniwake. Mpukutuwo unakonzedwa kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+