Mateyu 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Amene ali ndi makutu amve.+ Chivumbulutso 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Ali ndi makutu amve zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti:+ Wopambana pa nkhondo+ ndidzamupatsa ena mwa mana+ obisika. Ndidzamupatsanso mwala woyera wolembedwa dzina latsopano+ limene wina aliyense sakulidziwa kupatulapo wolandira yekhayo.’+ Chivumbulutso 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu+ ukunena ku mipingo.’+
17 “‘Ali ndi makutu amve zimene mzimu ukunena ku mipingo kuti:+ Wopambana pa nkhondo+ ndidzamupatsa ena mwa mana+ obisika. Ndidzamupatsanso mwala woyera wolembedwa dzina latsopano+ limene wina aliyense sakulidziwa kupatulapo wolandira yekhayo.’+